Yohane 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno anauza ogulitsa nkhundawo kuti: “Chotsani izi muno! Musiyiretu kusandutsa nyumba ya Atate wanga kukhala nyumba ya malonda!”*+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:16 Yesu—Ndi Njira, tsa. 43
16 Ndiyeno anauza ogulitsa nkhundawo kuti: “Chotsani izi muno! Musiyiretu kusandutsa nyumba ya Atate wanga kukhala nyumba ya malonda!”*+