Yohane 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ophunzira ake anakumbukira zimene Malemba amanena kuti: “Kudzipereka kwanga panyumba yanu kudzakhala ngati moto umene ukuyaka mumtima mwanga.”+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:17 Nsanja ya Olonda,12/15/2010, ptsa. 8-9
17 Ophunzira ake anakumbukira zimene Malemba amanena kuti: “Kudzipereka kwanga panyumba yanu kudzakhala ngati moto umene ukuyaka mumtima mwanga.”+