-
Yohane 3:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ngati ndakuuzani zinthu zapadziko lapansi koma inu simukukhulupirirabe, ndiye mungakhulupirire bwanji nditakuuzani zinthu zakumwamba?
-