-
Yohane 4:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Mayiyo anauza Yesu kuti: “Bambo, ndipatseni madzi amenewo, kuti ndisadzamvenso ludzu komanso kuti ndisamabwerenso kuno kudzatunga madzi.”
-