-
Yohane 4:38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Ine ndakutumizani kukakolola zimene simunakhetsere thukuta. Ena anagwira ntchito mwakhama ndipo inu mukupindula ndi ntchito imene iwo anagwira.”
-