Yohane 4:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 ndipo anauza mayi uja kuti: “Sikuti tikukhulupirira chifukwa cha mawu ako okha aja ayi, chifukwa tadzimvera tokha ndipo tikudziwa kuti munthu uyu ndi mpulumutsidi wa dziko.”+
42 ndipo anauza mayi uja kuti: “Sikuti tikukhulupirira chifukwa cha mawu ako okha aja ayi, chifukwa tadzimvera tokha ndipo tikudziwa kuti munthu uyu ndi mpulumutsidi wa dziko.”+