Yohane 4:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Choncho atafika ku Galileya, anthu a ku Galileyako anamulandira chifukwa anali ataona zonse zimene anachita pachikondwerero ku Yerusalemu,+ popeza nawonso anapita kuchikondwereroko.+
45 Choncho atafika ku Galileya, anthu a ku Galileyako anamulandira chifukwa anali ataona zonse zimene anachita pachikondwerero ku Yerusalemu,+ popeza nawonso anapita kuchikondwereroko.+