-
Yohane 4:47Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
47 Munthuyu atamva kuti Yesu wafika ku Galileya kuchokera ku Yudeya, anapita kwa iye kukamupempha kuti apite ku Kaperenao nʼkukachiritsa mwana wakeyo, chifukwa anali atatsala pangʼono kumwalira.
-