Yohane 4:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Choncho iye anawafunsa ola limene anachira ndipo iwo anamuyankha kuti: “Malungo* ake atha dzulo cha mʼma 1 koloko masana.”*
52 Choncho iye anawafunsa ola limene anachira ndipo iwo anamuyankha kuti: “Malungo* ake atha dzulo cha mʼma 1 koloko masana.”*