Yohane 5:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Koma ine ndili ndi umboni woposa wa Yohane, chifukwa ntchito zimene Atate wanga anandipatsa kuti ndizikwaniritse, ntchito zimene ndikuchitazi, zikuchitira umboni kuti Atate ananditumadi.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:36 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 16 Nsanja ya Olonda,1/15/2005, tsa. 113/15/1987, tsa. 8
36 Koma ine ndili ndi umboni woposa wa Yohane, chifukwa ntchito zimene Atate wanga anandipatsa kuti ndizikwaniritse, ntchito zimene ndikuchitazi, zikuchitira umboni kuti Atate ananditumadi.+
5:36 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 16 Nsanja ya Olonda,1/15/2005, tsa. 113/15/1987, tsa. 8