-
Yohane 6:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ndiyeno Yesu anatenga mitanda ya mkate ija. Atayamika, anaigawa kwa anthu onse amene anakhala pansi aja. Anachitanso chimodzimodzi ndi tinsomba tija ndipo anthuwo anadya mmene aliyense anafunira.
-