Yohane 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Komanso nyanja inayamba kuchita mafunde chifukwa kunkawomba mphepo yamphamvu.+