Yohane 6:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno iwo anamufunsa kuti: “Ndiye inuyo muchita chizindikiro chotani+ kuti ife tichione nʼkukukhulupirirani? Muchita ntchito yotani? Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:30 Yesu—Ndi Njira, tsa. 132 Nsanja ya Olonda,10/1/1987, tsa. 8
30 Ndiyeno iwo anamufunsa kuti: “Ndiye inuyo muchita chizindikiro chotani+ kuti ife tichione nʼkukukhulupirirani? Muchita ntchito yotani?