Yohane 6:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Chifuniro cha amene anandituma ine nʼchakuti, ndisataye aliyense mwa onse amene iye wandipatsa, koma kuti ndidzawaukitse+ pa tsiku lomaliza.
39 Chifuniro cha amene anandituma ine nʼchakuti, ndisataye aliyense mwa onse amene iye wandipatsa, koma kuti ndidzawaukitse+ pa tsiku lomaliza.