Yohane 6:64 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Koma pali ena mwa inu amene sakukhulupirira.” Kuchokera pachiyambi, Yesu ankadziwa amene sankakhulupirira komanso amene adzamupereke.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:64 Nsanja ya Olonda,4/15/2008, tsa. 3110/15/1987, tsa. 9 Kukambitsirana, tsa. 119
64 Koma pali ena mwa inu amene sakukhulupirira.” Kuchokera pachiyambi, Yesu ankadziwa amene sankakhulupirira komanso amene adzamupereke.+