Yohane 6:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 Kwenikweni ankanena za Yudasi mwana wa Simoni Isikariyoti, chifukwa ameneyu anali kudzamupereka, ngakhale kuti anali mmodzi wa ophunzira 12 aja.+
71 Kwenikweni ankanena za Yudasi mwana wa Simoni Isikariyoti, chifukwa ameneyu anali kudzamupereka, ngakhale kuti anali mmodzi wa ophunzira 12 aja.+