Yohane 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Wolankhula zamʼmaganizo mwake amadzifunira yekha ulemerero. Koma wofunira ulemerero iye amene anamutuma,+ ameneyu ndi woona ndipo mwa iye mulibe chosalungama. Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:18 Nsanja ya Olonda,5/1/2006, ptsa. 24-252/1/1996, tsa. 10
18 Wolankhula zamʼmaganizo mwake amadzifunira yekha ulemerero. Koma wofunira ulemerero iye amene anamutuma,+ ameneyu ndi woona ndipo mwa iye mulibe chosalungama.