-
Yohane 8:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Nʼchifukwa chake ndakuuzani kuti: Inu mudzafa mudakali ochimwa. Chifukwa ngati simukukhulupirira kuti amene munkamuyembekezera uja ndi ine, mudzafa mudakali ochimwa.”
-