Yohane 8:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Yesu anawauza kuti: “Mulungu akanakhala Atate wanu, mukanandikonda,+ chifukwa ine ndinachokera kwa Mulungu ndipo ndili pano. Sindinabwere mwakufuna kwanga koma Iyeyo ndi amene anandituma.+
42 Yesu anawauza kuti: “Mulungu akanakhala Atate wanu, mukanandikonda,+ chifukwa ine ndinachokera kwa Mulungu ndipo ndili pano. Sindinabwere mwakufuna kwanga koma Iyeyo ndi amene anandituma.+