Yohane 8:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Chikhalirecho simukumudziwa,+ koma ine ndikumudziwa.+ Ngati ndinganene kuti sindikumudziwa ndingakhale wabodza ngati inu. Koma ndikumudziwa ndithu ndipo ndikusunga mawu ake.
55 Chikhalirecho simukumudziwa,+ koma ine ndikumudziwa.+ Ngati ndinganene kuti sindikumudziwa ndingakhale wabodza ngati inu. Koma ndikumudziwa ndithu ndipo ndikusunga mawu ake.