Yohane 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Atanena zimenezi, analavulira malovu pansi nʼkukanda matope ndi malovuwo, kenako anapaka matopewo mʼmaso mwa munthuyo.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:6 Muzikonda Anthu, lesson 3
6 Atanena zimenezi, analavulira malovu pansi nʼkukanda matope ndi malovuwo, kenako anapaka matopewo mʼmaso mwa munthuyo.+