Yohane 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno anamuuza kuti: “Pita ukasambe mʼdziwe la Siloamu” (dzina limene kumasulira kwake ndi “Otumizidwa”). Choncho anapita kukasamba ndipo anabwerako akuona.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:7 Muzikonda Anthu, lesson 3
7 Ndiyeno anamuuza kuti: “Pita ukasambe mʼdziwe la Siloamu” (dzina limene kumasulira kwake ndi “Otumizidwa”). Choncho anapita kukasamba ndipo anabwerako akuona.+