Yohane 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye anayankha kuti: “Munthu wina dzina lake Yesu anakanda matope nʼkuwapaka mʼmaso mwangamu. Kenako anandiuza kuti, ‘Pita ku Siloamu ukasambe.’+ Ndiye ndinapitadi kukasamba ndipo ndayamba kuona.”
11 Iye anayankha kuti: “Munthu wina dzina lake Yesu anakanda matope nʼkuwapaka mʼmaso mwangamu. Kenako anandiuza kuti, ‘Pita ku Siloamu ukasambe.’+ Ndiye ndinapitadi kukasamba ndipo ndayamba kuona.”