-
Yohane 9:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Afarisiwo anafunsanso munthu amene anali wosaona uja kuti: “Nanga iwe ukuti bwanji za munthu ameneyu, popeza kuti wakutsegula maso?” Munthuyo anati: “Ndi mneneri.”
-