Yohane 9:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ndiyeno Yesu ananena kuti: “Ndinabwera mʼdziko lino kudzapereka chiweruzo chakuti, osaona ayambe kuona+ ndipo amene akuona akhale osaona.”+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:39 Nsanja ya Olonda,8/1/1988, tsa. 31
39 Ndiyeno Yesu ananena kuti: “Ndinabwera mʼdziko lino kudzapereka chiweruzo chakuti, osaona ayambe kuona+ ndipo amene akuona akhale osaona.”+