Yohane 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iwo anapita kwa Filipo+ amene kwawo kunali ku Betsaida wa ku Galileya, ndipo anayamba kumupempha kuti: “Bambo, ife tikufuna tione Yesu.” Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:21 Nsanja ya Olonda,10/15/2015, tsa. 21
21 Iwo anapita kwa Filipo+ amene kwawo kunali ku Betsaida wa ku Galileya, ndipo anayamba kumupempha kuti: “Bambo, ife tikufuna tione Yesu.”