Yohane 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Aliyense amene amakonda moyo wake akuuwononga, koma aliyense amene amadana ndi moyo wake+ mʼdziko lino akuuteteza kuti adzapeze moyo wosatha.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:25 Mtendere Weniweni, tsa. 162
25 Aliyense amene amakonda moyo wake akuuwononga, koma aliyense amene amadana ndi moyo wake+ mʼdziko lino akuuteteza kuti adzapeze moyo wosatha.+