Yohane 12:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ngati munthu akufuna kunditumikira anditsatire ndipo kumene ine ndidzakhale, mtumiki wanga adzakhalanso komweko.+ Aliyense wonditumikira ine, Atate adzamulemekeza. Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:26 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 240-241 Nsanja ya Olonda,11/15/1989, tsa. 9
26 Ngati munthu akufuna kunditumikira anditsatire ndipo kumene ine ndidzakhale, mtumiki wanga adzakhalanso komweko.+ Aliyense wonditumikira ine, Atate adzamulemekeza.