Yohane 12:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Yesu anawauza kuti: “Kuwala kukhalabe pakati panu kanthawi pangʼono. Yendani pamene kuwalako mudakali nako, kuti mdima usakugwereni. Aliyense amene akuyenda mumdima sadziwa kumene akupita.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:35 Yesu—Ndi Njira, tsa. 242
35 Yesu anawauza kuti: “Kuwala kukhalabe pakati panu kanthawi pangʼono. Yendani pamene kuwalako mudakali nako, kuti mdima usakugwereni. Aliyense amene akuyenda mumdima sadziwa kumene akupita.+