Yohane 12:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pamene kuwala mudakali nako, sonyezani kuti mukukhulupirira kuwalako, kuti mukhale ana ake a kuwala.”+ Yesu atanena zimenezi, anachoka nʼkukabisala. Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:36 Yesu—Ndi Njira, tsa. 242 Nsanja ya Olonda,4/15/2008, tsa. 3212/1/1989, tsa. 8
36 Pamene kuwala mudakali nako, sonyezani kuti mukukhulupirira kuwalako, kuti mukhale ana ake a kuwala.”+ Yesu atanena zimenezi, anachoka nʼkukabisala.