Yohane 13:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Popeza Yudasi ankasunga bokosi la ndalama,+ ena ankaganiza kuti Yesu ankamuuza kuti, “Ugule zinthu zonse zimene zikufunikira pachikondwerero,” kapena kuti apereke kenakake kwa osauka.
29 Popeza Yudasi ankasunga bokosi la ndalama,+ ena ankaganiza kuti Yesu ankamuuza kuti, “Ugule zinthu zonse zimene zikufunikira pachikondwerero,” kapena kuti apereke kenakake kwa osauka.