Yohane 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiye ndikapita kukakukonzerani malowo, ndidzabweranso kudzakutengerani kwathu, kuti kumene ine ndikakhale inunso mukakhale komweko.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:3 Nsanja ya Olonda,11/15/1994, ptsa. 4-56/15/1994, tsa. 6 Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 142
3 Ndiye ndikapita kukakukonzerani malowo, ndidzabweranso kudzakutengerani kwathu, kuti kumene ine ndikakhale inunso mukakhale komweko.+