-
Yohane 14:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Aliyense amene ali ndi malamulo anga ndipo amawatsatira, ndi amene amandikonda. Komanso amene amandikonda, Atate wanga adzamukondanso. Inenso ndidzamukonda ndipo ndidzadzionetsera bwinobwino kwa iye.”
-