Yohane 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mukhale ogwirizana ndi ine ndipo inenso ndikhala wogwirizana ndi inu. Mofanana ndi nthambi imene singabereke zipatso payokha, pokhapokha ngati ili yolumikizikabe kumpesawo, inunso simungabereke zipatso pokhapokha ngati muli olumikizika kwa ine.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:4 Yesu—Ndi Njira, tsa. 276 Nsanja ya Olonda,2/1/2002, tsa. 18
4 Mukhale ogwirizana ndi ine ndipo inenso ndikhala wogwirizana ndi inu. Mofanana ndi nthambi imene singabereke zipatso payokha, pokhapokha ngati ili yolumikizikabe kumpesawo, inunso simungabereke zipatso pokhapokha ngati muli olumikizika kwa ine.+