-
Yohane 15:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ngati munthu sapitiriza kukhala wolumikizika kwa ine, amaponyedwa kunja ngati nthambi ndipo amauma. Anthu amasonkhanitsa nthambi zoterozo nʼkuziponya pamoto ndipo zimapsa.
-