Yohane 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndakuuzani zinthu zimenezi kuti mukhale ndi chimwemwe chimene ine ndili nacho komanso kuti chimwemwe chanu chisefukire.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:11 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2018, tsa. 20
11 Ndakuuzani zinthu zimenezi kuti mukhale ndi chimwemwe chimene ine ndili nacho komanso kuti chimwemwe chanu chisefukire.+