Yohane 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Si inu amene munandisankha, koma ine ndinakusankhani kuti mupitirize kubereka zipatso zochuluka, komanso kuti zipatso zanuzo zisathe, kuti chilichonse chimene mungapemphe Atate mʼdzina langa akupatseni.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:16 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2018, tsa. 21
16 Si inu amene munandisankha, koma ine ndinakusankhani kuti mupitirize kubereka zipatso zochuluka, komanso kuti zipatso zanuzo zisathe, kuti chilichonse chimene mungapemphe Atate mʼdzina langa akupatseni.+