-
Yohane 16:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Ndalankhula zimenezi kwa inu mʼmafanizo. Nthawi ikubwera pamene sindidzalankhulanso ndi inu pogwiritsa ntchito mafanizo, koma ndidzakuuzani za Atate momveka bwino.
-