Yohane 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yesu atalankhula zinthu zimenezi, anakweza maso ake kumwamba nʼkunena kuti: “Atate, nthawi yafika. Lemekezani mwana wanu, kuti mwana wanu akulemekezeni.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:1 Yesu—Ndi Njira, tsa. 280 Nsanja ya Olonda,10/15/2013, tsa. 27
17 Yesu atalankhula zinthu zimenezi, anakweza maso ake kumwamba nʼkunena kuti: “Atate, nthawi yafika. Lemekezani mwana wanu, kuti mwana wanu akulemekezeni.+