Yohane 17:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndawapatsa ulemerero umene munandipatsa, kuti iwo akhale amodzi ngati mmene ifenso tilili amodzi.+
22 Ndawapatsa ulemerero umene munandipatsa, kuti iwo akhale amodzi ngati mmene ifenso tilili amodzi.+