Yohane 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atate, ine ndikufuna kuti amene mwandipatsawa adzakhale limodzi ndi ine kumene ine ndidzakhale,+ kuti adzaone ulemerero wanga umene inu mwandipatsa, chifukwa munandikonda musanayale maziko a dziko.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:24 Yesu—Ndi Njira, tsa. 281 Nsanja ya Olonda,10/15/2013, tsa. 309/15/1990, tsa. 9
24 Atate, ine ndikufuna kuti amene mwandipatsawa adzakhale limodzi ndi ine kumene ine ndidzakhale,+ kuti adzaone ulemerero wanga umene inu mwandipatsa, chifukwa munandikonda musanayale maziko a dziko.+