Yohane 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho Yudasi anatenga gulu la asilikali komanso alonda ochokera kwa ansembe aakulu ndi kwa Afarisi. Iwo anafika kumeneko atanyamula miyuni, nyale ndi zida.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:3 Yesu—Ndi Njira, tsa. 284 Nsanja ya Olonda,10/15/1990, tsa. 8
3 Choncho Yudasi anatenga gulu la asilikali komanso alonda ochokera kwa ansembe aakulu ndi kwa Afarisi. Iwo anafika kumeneko atanyamula miyuni, nyale ndi zida.+