Yohane 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yesu anamuyankha kuti: “Ndalankhula poyera ku dzikoli. Nthawi zonse ndinkaphunzitsa mʼmasunagoge ndi mʼkachisi,+ kumene Ayuda onse ankasonkhana, ndipo sindinalankhule chilichonse kumbali.
20 Yesu anamuyankha kuti: “Ndalankhula poyera ku dzikoli. Nthawi zonse ndinkaphunzitsa mʼmasunagoge ndi mʼkachisi,+ kumene Ayuda onse ankasonkhana, ndipo sindinalankhule chilichonse kumbali.