Yohane 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiye ankapita kwa iye nʼkumanena kuti: “Moni, inu Mfumu ya Ayuda!” Komanso ankamumenya makofi kumaso.+
3 Ndiye ankapita kwa iye nʼkumanena kuti: “Moni, inu Mfumu ya Ayuda!” Komanso ankamumenya makofi kumaso.+