Yohane 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pilato anatulukanso kunja nʼkuwauza kuti: “Onani! ndimutulutsa panja pano kwa inu, kuti mudziwe kuti sindinamupeze ndi mlandu.”+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:4 Yesu—Ndi Njira, tsa. 295 Nsanja ya Olonda,1/1/1991, tsa. 9
4 Pilato anatulukanso kunja nʼkuwauza kuti: “Onani! ndimutulutsa panja pano kwa inu, kuti mudziwe kuti sindinamupeze ndi mlandu.”+