-
Yohane 19:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Choncho Yesu anatuluka panja atavala chisoti chachifumu chaminga chija ndi malaya akunja apepo. Ndiyeno Pilato anawauza kuti: “Taonani! Mwamuna uja ndi uyu!”
-