Yohane 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma pamene ansembe aakulu ndi alonda anamuona, anafuula kuti: “Apachikidwe ameneyo! Apachikidwe ameneyo!”*+ Pilato anawauza kuti: “Mutengeni mukamupachike nokha,* chifukwa ine sindinamupeze ndi mlandu uliwonse.”+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:6 Nsanja ya Olonda,1/15/1991, tsa. 87/1/1988, tsa. 31
6 Koma pamene ansembe aakulu ndi alonda anamuona, anafuula kuti: “Apachikidwe ameneyo! Apachikidwe ameneyo!”*+ Pilato anawauza kuti: “Mutengeni mukamupachike nokha,* chifukwa ine sindinamupeze ndi mlandu uliwonse.”+