Yohane 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako anamupereka kwa iwo kuti akamuphe pomupachika pamtengo.+ Tsopano Yesu anali mʼmanja mwawo.