Yohane 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pilato analembanso dzina laudindo nʼkuliika pamtengo wozunzikirapowo.* Analemba kuti: “Yesu Mnazareti, Mfumu ya Ayuda.”+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:19 Yesu—Ndi Njira, tsa. 298 Nsanja ya Olonda,2/1/1991, tsa. 8
19 Pilato analembanso dzina laudindo nʼkuliika pamtengo wozunzikirapowo.* Analemba kuti: “Yesu Mnazareti, Mfumu ya Ayuda.”+