Yohane 19:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pamalopo panali mtsuko wodzaza vinyo wowawasa. Choncho anatenga siponji nʼkuiviika muvinyo wowawasayo ndipo anaisomeka kukamtengo ka hisope* nʼkuifikitsa pakamwa pake.+
29 Pamalopo panali mtsuko wodzaza vinyo wowawasa. Choncho anatenga siponji nʼkuiviika muvinyo wowawasayo ndipo anaisomeka kukamtengo ka hisope* nʼkuifikitsa pakamwa pake.+